Yeaheiyeah
When I was searching, I thought I'd never find you my darlin'
Now that you're here, ine ndigwilisa tu my darlin'
Love is tricky but I'm willing to try for you darlin'
You should know
Ukapita, n'zapenga misala
A'nzangawa, azayesa ndadwala
Ukachoka, n'zasowa chonena
Palibe azandikwanise kutonthoza
Hm, ndanena
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ayi ndimangeni, lock me up baby
Come keep me in your arms, undigwilise
Oouu, I don't wanna go nowhere
Oouu, Girl I'm happy here
Oouu, ndikuziwise
What will happen if you
Ukapita, n'zapenga misala
Anzangawa, azayesa ndadwala
Ukachoka, n'zasowa chonena
Palibe azandikwanise kutonthoza
Hm, ndanena
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ndinene ine ndinene
Ukapita, n'zapenga misala
Anzangawa, azayesa ndadwala
Ukachoka, n'zasowa chonena
Palibe azandikwanise kutonthoza
Hm ndanena