See this smile you been making, girl no mistake
I'm yours for the takin'
I need you beside me, you know I dey try to
Forget all your love, your kisses, your time maybe I can focus
Still it no go work for me, what did you do?
Ati chikondi chimasuluka, nthawi ikamadusa
Why do I feel the same? Like I fell for you yesterday
Mai ntima unasankha, mpaka kudwala ukapanda
Kulemba message, my girl you got me
See I'm drowning, falling
Kukukonda iwe, kuhopela iwe
Ndinasankha iwe
Ntima wanga n'gofuntha
Uyimira iwe, napenga pa iwe
Ndinasankha iwe
Ati chikondi no ceiling, mpaka kumwamba
Uziwiletu, mpaka mathelo
You dey on my mind long time so forgive
(Mami we can be together, palibe oletsa)
You're what I came for, chifukwa cha iweyo
My angel my m'ngelo, see you dey rise my flame
(Akati)
Love is two people, ankanena ine ndi iweyo
See for you I'll travel for hours, days no matter nabola ndikupeze
Tisangalale
Ehh
Ehh
Ahhh-ahh-ahh-ahh-ahh
See I'm drowning, falling
Kukukonda iwe, kuhopela iwe
Ndinasankha iwe
Ntima wanga n'gofuntha
Uyimira iwe, napenga pa iwe
Ndinasankha iwe
Ohhh uuuhh
See I'm drowning, falling
Kukukonda iwe, kuhopela iwe
Ndinasankha iwe
Ntima wanga n'gofuntha
Uyimira iwe, napenga pa iwe
Ndinasankha iwe